Machitidwe 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popitiriza ulendo wawo m’mizinda, anali kupatsa okhulupirira a kumeneko malamulo oyenera kuwatsatira, malinga ndi zimene atumwi ndi akulu ku Yerusalemu anagamula.+
4 Popitiriza ulendo wawo m’mizinda, anali kupatsa okhulupirira a kumeneko malamulo oyenera kuwatsatira, malinga ndi zimene atumwi ndi akulu ku Yerusalemu anagamula.+