Machitidwe 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ndipo atamupeza anabwera naye ku Antiokeya. Choncho iwo anasonkhana ndi mpingo kumeneko chaka chonse, ndipo anaphunzitsa anthu ambirimbiri. Ku Antiokeya, n’kumene ophunzirawo anayamba kutchedwa Akhristu, motsogoleredwa ndi Mulungu.+
26 ndipo atamupeza anabwera naye ku Antiokeya. Choncho iwo anasonkhana ndi mpingo kumeneko chaka chonse, ndipo anaphunzitsa anthu ambirimbiri. Ku Antiokeya, n’kumene ophunzirawo anayamba kutchedwa Akhristu, motsogoleredwa ndi Mulungu.+