Machitidwe 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tinayamba ulendo wa panyanja ku Filipi masiku a mkate wopanda chofufumitsa atatha.+ Ndipo tinawapeza ku Torowa+ patapita masiku asanu. Kumeneko tinakhalako masiku 7.
6 Koma tinayamba ulendo wa panyanja ku Filipi masiku a mkate wopanda chofufumitsa atatha.+ Ndipo tinawapeza ku Torowa+ patapita masiku asanu. Kumeneko tinakhalako masiku 7.