-
Machitidwe 10:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Tsiku linalo anafika ku Kaisareya. Kumeneko Koneliyo anali kuwayembekezera, ndipo anasonkhanitsa achibale ndi mabwenzi ake apamtima.
-