Yohane 5:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Inu mumafufuza m’Malemba,+ chifukwa mumaganiza kuti kudzera m’Malembawo mudzapeza moyo wosatha, ndipo Malemba omwewo ndi amenenso amachitira umboni za ine.+
39 “Inu mumafufuza m’Malemba,+ chifukwa mumaganiza kuti kudzera m’Malembawo mudzapeza moyo wosatha, ndipo Malemba omwewo ndi amenenso amachitira umboni za ine.+