Machitidwe 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mmodzi wa iwo dzina lake Agabo,+ analosera mwa mzimu kuti padziko lonse lapansi kumene kuli anthu,+ padzagwa njala yaikulu. Izi zinachitikadi m’nthawi ya Kalaudiyo.
28 Mmodzi wa iwo dzina lake Agabo,+ analosera mwa mzimu kuti padziko lonse lapansi kumene kuli anthu,+ padzagwa njala yaikulu. Izi zinachitikadi m’nthawi ya Kalaudiyo.