1 Petulo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa chakuti simukupitiriza kuthamanga nawo limodzi m’chithaphwi cha makhalidwe oipa,+ anthu a m’dzikoli sakumvetsa, choncho amakunyozani.+
4 Chifukwa chakuti simukupitiriza kuthamanga nawo limodzi m’chithaphwi cha makhalidwe oipa,+ anthu a m’dzikoli sakumvetsa, choncho amakunyozani.+