Yeremiya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo adzamenyana nawe ndithu, koma sadzapambana,+ pakuti Yehova wanena kuti, ‘Ine ndili ndi iwe+ kuti ndikulanditse.’”+ Mateyu 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ndi kuwaphunzitsa+ kusunga+ zinthu zonse zimene ndinakulamulirani.+ Ndipo dziwani kuti ine ndili pamodzi ndi inu+ masiku onse mpaka m’nyengo ya mapeto a nthawi* ino.”+
19 Iwo adzamenyana nawe ndithu, koma sadzapambana,+ pakuti Yehova wanena kuti, ‘Ine ndili ndi iwe+ kuti ndikulanditse.’”+
20 ndi kuwaphunzitsa+ kusunga+ zinthu zonse zimene ndinakulamulirani.+ Ndipo dziwani kuti ine ndili pamodzi ndi inu+ masiku onse mpaka m’nyengo ya mapeto a nthawi* ino.”+