Machitidwe 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma mabwana ake aja ataona kuti chiyembekezo chawo chopeza phindu chatha,+ anagwira Paulo ndi Sila ndi kuwakokera mumsika, kubwalo la olamulira.+
19 Koma mabwana ake aja ataona kuti chiyembekezo chawo chopeza phindu chatha,+ anagwira Paulo ndi Sila ndi kuwakokera mumsika, kubwalo la olamulira.+