Machitidwe 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera chilango cha imfa kapena kuponyedwa m’ndende.+ Machitidwe 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo anali kungotsutsana naye nkhani zokhudzana ndi kulambira+ kwawo mulungu, ndi za munthu wina wake wotchedwa Yesu amene anafa koma Paulo akupitiriza kunena motsimikiza kuti ali moyo.+
29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera chilango cha imfa kapena kuponyedwa m’ndende.+
19 Iwo anali kungotsutsana naye nkhani zokhudzana ndi kulambira+ kwawo mulungu, ndi za munthu wina wake wotchedwa Yesu amene anafa koma Paulo akupitiriza kunena motsimikiza kuti ali moyo.+