1 Akorinto 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ineyo ndinabzala,+ Apolo anathirira,+ koma Mulungu ndiye anakulitsa.+