Machitidwe 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kukamupempha zikalata za chilolezo zopita nazo kumasunagoge a ku Damasiko. Anapempha zikalatazo kuti akakapeza wina aliyense wotsatira Njirayo,*+ mwamuna kapena mkazi, akabwere naye ku Yerusalemu ali womangidwa. Machitidwe 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinazunza otsatira Njira imeneyi mpaka imfa.+ Ndinali kumanga amuna ndi akazi ndi kuwapereka kundende.+
2 kukamupempha zikalata za chilolezo zopita nazo kumasunagoge a ku Damasiko. Anapempha zikalatazo kuti akakapeza wina aliyense wotsatira Njirayo,*+ mwamuna kapena mkazi, akabwere naye ku Yerusalemu ali womangidwa.
4 Ndinazunza otsatira Njira imeneyi mpaka imfa.+ Ndinali kumanga amuna ndi akazi ndi kuwapereka kundende.+