2 Atesalonika 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi imene Ambuye Yesu adzaonekere*+ kuchokera kumwamba limodzi ndi angelo ake amphamvu+ m’moto walawilawi, inuyo amene panopo mukuvutika mudzapeza mpumulo pamodzi nafe.
7 Pa nthawi imene Ambuye Yesu adzaonekere*+ kuchokera kumwamba limodzi ndi angelo ake amphamvu+ m’moto walawilawi, inuyo amene panopo mukuvutika mudzapeza mpumulo pamodzi nafe.