Aefeso 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Muzikumbukiranso kuti pa nthawi imene ija munali opanda Khristu,+ otalikirana+ ndi mtundu wa Isiraeli komanso alendo osadziwika pa mapangano a lonjezolo.+ Munalibe chiyembekezo+ ndipo inu munalibe Mulungu m’dzikoli.+ Akolose 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiponso, ngakhale kuti munali akufa m’machimo anu ndipo munali osadulidwa, Mulungu anakupatsani moyo kuti mukhale ogwirizana ndi Khristu,+ ndipo anatikhululukira machimo athu onse motikomera mtima.+
12 Muzikumbukiranso kuti pa nthawi imene ija munali opanda Khristu,+ otalikirana+ ndi mtundu wa Isiraeli komanso alendo osadziwika pa mapangano a lonjezolo.+ Munalibe chiyembekezo+ ndipo inu munalibe Mulungu m’dzikoli.+
13 Ndiponso, ngakhale kuti munali akufa m’machimo anu ndipo munali osadulidwa, Mulungu anakupatsani moyo kuti mukhale ogwirizana ndi Khristu,+ ndipo anatikhululukira machimo athu onse motikomera mtima.+