Malaki 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kodi munthu wochokera kufumbi angabere Mulungu? Komatu inu mukundibera.” Inu mukunena kuti: “Takuberani motani?” “Mukundibera kudzera m’chakhumi* ndi m’zopereka.
8 “Kodi munthu wochokera kufumbi angabere Mulungu? Komatu inu mukundibera.” Inu mukunena kuti: “Takuberani motani?” “Mukundibera kudzera m’chakhumi* ndi m’zopereka.