Aefeso 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero nthawi zonse muzikumbukira kuti poyamba munali anthu a mitundu ina mwakuthupi.+ Anthu otchedwa “odulidwa,” amene anadulidwa mwakuthupi ndi manja,+ anali kukutchani “osadulidwa.”
11 Chotero nthawi zonse muzikumbukira kuti poyamba munali anthu a mitundu ina mwakuthupi.+ Anthu otchedwa “odulidwa,” amene anadulidwa mwakuthupi ndi manja,+ anali kukutchani “osadulidwa.”