Aheberi 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choteronso, kuchokera mwa mwamuna mmodzi,+ amene anali ngati wakufa,+ kunabadwa ana ochuluka ngati nyenyezi zakumwamba komanso osawerengeka ngati mchenga wa m’mbali mwa nyanja.+
12 Choteronso, kuchokera mwa mwamuna mmodzi,+ amene anali ngati wakufa,+ kunabadwa ana ochuluka ngati nyenyezi zakumwamba komanso osawerengeka ngati mchenga wa m’mbali mwa nyanja.+