Machitidwe 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Mulungu anamuukitsa+ kwa akufa mwa kumasula zopweteka za imfa,+ chifukwa zinali zosatheka kuti imfa ipitirize kumugwira mwamphamvu.+ Machitidwe 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa.+ 1 Petulo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 amene kudzera mwa iye, mukukhulupirira Mulungu,+ amene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kum’patsa ulemerero,+ kuti chikhulupiriro ndiponso chiyembekezo chanu zikhale mwa Mulungu.+
24 Koma Mulungu anamuukitsa+ kwa akufa mwa kumasula zopweteka za imfa,+ chifukwa zinali zosatheka kuti imfa ipitirize kumugwira mwamphamvu.+
21 amene kudzera mwa iye, mukukhulupirira Mulungu,+ amene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kum’patsa ulemerero,+ kuti chikhulupiriro ndiponso chiyembekezo chanu zikhale mwa Mulungu.+