Aroma 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye anaperekedwa chifukwa cha machimo athu+ ndipo anaukitsidwa kuti tiyesedwe olungama.+