1 Akorinto 15:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Mphamvu+ imene imabala imfa ndiyo uchimo, koma mphamvu ya uchimo ndi Chilamulo.+