1 Akorinto 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kwa anthu opanda chilamulo+ ndinakhala ngati wopanda chilamulo,+ kuti ndipindule anthu opanda chilamulo. Ngakhale zili choncho, sikuti ndine wopanda chilamulo+ kwa Mulungu koma ndili pansi pa chilamulo kwa Khristu.+
21 Kwa anthu opanda chilamulo+ ndinakhala ngati wopanda chilamulo,+ kuti ndipindule anthu opanda chilamulo. Ngakhale zili choncho, sikuti ndine wopanda chilamulo+ kwa Mulungu koma ndili pansi pa chilamulo kwa Khristu.+