Aroma 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma tikuyamika Mulungu kuti ngakhale poyamba munali akapolo a uchimo, munamvera mochokera pansi pa mtima mtundu wa chiphunzitso chimene chinaperekedwa kwa inu.+ 1 Akorinto 15:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Koma Mulungu ayamikike, pakuti amatithandiza kuti tipambane kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu.+
17 Koma tikuyamika Mulungu kuti ngakhale poyamba munali akapolo a uchimo, munamvera mochokera pansi pa mtima mtundu wa chiphunzitso chimene chinaperekedwa kwa inu.+
57 Koma Mulungu ayamikike, pakuti amatithandiza kuti tipambane kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu.+