Yohane 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndithudi ndikukuuzani, Iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira amene anandituma ine ali nawo moyo wosatha,+ ndipo salowa m’chiweruzo koma wachoka ku imfa, waolokera ku moyo.+
24 Ndithudi ndikukuuzani, Iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira amene anandituma ine ali nawo moyo wosatha,+ ndipo salowa m’chiweruzo koma wachoka ku imfa, waolokera ku moyo.+