1 Timoteyo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kwa Mfumu yamuyaya,+ imene siifa,+ yosaoneka,+ yekhayo amene ali Mulungu,+ kwa iyeyo kupite ulemu ndi ulemerero mpaka muyaya.+ Ame. Aheberi 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mwa chikhulupiriro anachoka mu Iguputo,+ koma osati chifukwa choopa mfumu ayi,+ pakuti anapitiriza kupirira moleza mtima ngati kuti akuona Wosaonekayo.+
17 Kwa Mfumu yamuyaya,+ imene siifa,+ yosaoneka,+ yekhayo amene ali Mulungu,+ kwa iyeyo kupite ulemu ndi ulemerero mpaka muyaya.+ Ame.
27 Mwa chikhulupiriro anachoka mu Iguputo,+ koma osati chifukwa choopa mfumu ayi,+ pakuti anapitiriza kupirira moleza mtima ngati kuti akuona Wosaonekayo.+