Miyambo 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chinthu chimene unali kuyembekeza chikalephereka, chimadwalitsa mtima.+ Koma chomwe unali kufuna chikachitika, chimakhala ngati mtengo wa moyo.+
12 Chinthu chimene unali kuyembekeza chikalephereka, chimadwalitsa mtima.+ Koma chomwe unali kufuna chikachitika, chimakhala ngati mtengo wa moyo.+