1 Akorinto 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma aliyense pamalo pake: Choyamba Khristu, amene ndi chipatso choyambirira,+ kenako ake a Khristu pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake.
23 Koma aliyense pamalo pake: Choyamba Khristu, amene ndi chipatso choyambirira,+ kenako ake a Khristu pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake.