23 Ine wogwirizana ndi iwo, inu wogwirizana ndi ine, kuti iwo akhale mu umodzi weniweni,+ kuti dziko lidziwe kuti inu munandituma ine, ndi kuti munawakonda iwo mmene munandikondera ine.
24 ndi kuvala+ umunthu watsopano+ umene unalengedwa+ mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndipo umatsatira zofunika pa chilungamo chenicheni+ ndi pa kukhulupirika.