Genesis 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Potsirizira pake, masiku oti Rabeka abereke anakwana, ndipo m’mimba mwake munali mapasa.+