Aroma 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tikudziwa tsopano kuti Mulungu amagwirizanitsa zochita zake zonse+ pofuna kupindulitsa amene amakonda Mulungu, anthu oitanidwa mogwirizana ndi cholinga chake.+ Aheberi 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso, munthu amalandira ulemu umenewu, osati mwa kufuna kwake,+ koma mwa kuchita kuitanidwa ndi Mulungu,+ monga mmene anaitanira Aroni.+
28 Tikudziwa tsopano kuti Mulungu amagwirizanitsa zochita zake zonse+ pofuna kupindulitsa amene amakonda Mulungu, anthu oitanidwa mogwirizana ndi cholinga chake.+
4 Komanso, munthu amalandira ulemu umenewu, osati mwa kufuna kwake,+ koma mwa kuchita kuitanidwa ndi Mulungu,+ monga mmene anaitanira Aroni.+