2 Timoteyo 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’nyumba yaikulu simukhala ziwiya zagolide ndi zasiliva zokha ayi, koma mumakhalanso zamtengo ndi zadothi. Ziwiya zina zimakhala za ntchito yolemekezeka koma zina zimakhala za ntchito yonyozeka.+
20 M’nyumba yaikulu simukhala ziwiya zagolide ndi zasiliva zokha ayi, koma mumakhalanso zamtengo ndi zadothi. Ziwiya zina zimakhala za ntchito yolemekezeka koma zina zimakhala za ntchito yonyozeka.+