Luka 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Aliyense wogwera pamwala umenewo adzaphwanyika.+ Ndipo aliyense amene mwalawo udzamugwere,+ udzam’pereratu.”+ 1 Akorinto 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 koma ife timalalikira za Khristu amene anapachikidwa.+ Kwa Ayuda, chimenechi ndi chinthu chokhumudwitsa+ ndipo kwa mitundu ina ndi kupusa.+
18 Aliyense wogwera pamwala umenewo adzaphwanyika.+ Ndipo aliyense amene mwalawo udzamugwere,+ udzam’pereratu.”+
23 koma ife timalalikira za Khristu amene anapachikidwa.+ Kwa Ayuda, chimenechi ndi chinthu chokhumudwitsa+ ndipo kwa mitundu ina ndi kupusa.+