Levitiko 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Usagone ndi mwamuna+ mmene umagonera ndi mkazi.+ N’chonyansa chimenechi. Aefeso 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti zimene iwo amachita mseri n’zochititsa manyazi ngakhale kuzitchula.+