Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Musaganize kuti ndinabwera kudzawononga Chilamulo+ kapena Zolemba za aneneri. Sindinabwere kudzaziwononga koma kudzazikwaniritsa.+

  • Aroma 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma tsopano tamasulidwa ku Chilamulo,+ chifukwa tafa+ ku chilamulo chimene chinali kutimanga chija, kuti tikhale akapolo+ m’njira yatsopano motsogoleredwa ndi mzimu,+ osati m’njira yakale motsogoleredwa ndi malamulo olembedwa.+

  • Aefeso 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndi thupi lake,+ anathetsa chidani chimene chinalipo,+ chimene ndi Chilamulo chokhala ndi malamulo operekedwa monga malangizo.+ Anachithetsa kuti mogwirizana ndi iye, alenge munthu mmodzi watsopano+ kuchokera ku magulu awiri a anthu,+ ndi kukhazikitsa mtendere.

  • Akolose 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anafafanizanso+ chikalata cholembedwa ndi manja,+ chokhala ndi malamulo+ operekedwa monga malangizo, chimene chinali kutitsutsa.+ Ndipo Iye wachichotsa mwa kuchikhomera+ pamtengo wozunzikirapo.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena