Machitidwe 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iwo anati: “Khulupirira mwa Ambuye Yesu ndipo udzapulumuka,+ limodzi ndi a m’nyumba yako.”+