Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 15:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Muzipereka kwa Yehova ufa wamisere wa zipatso zanu zoyambirira ku mibadwo yanu yonse.

  • Nehemiya 10:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Komanso tinafunika kupititsa ufa woyambirira wamisere,+ zopereka zathu,+ zipatso za mtengo uliwonse,+ vinyo watsopano+ ndi mafuta+ kwa ansembe kumalo odyera+ m’nyumba ya Mulungu wathu. Tinafunikanso kupititsa chakhumi kwa Alevi+ pa zinthu zochokera m’nthaka yathu, pakuti Aleviwo anali kulandira chakhumi kuchokera m’mizinda yathu yonse ya zaulimi.

  • Ezekieli 44:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Zipatso zonse zabwino kwambiri zoyambirira za mtundu uliwonse ndi zopereka zanu zonse za mtundu uliwonse zabwino kwambiri zidzakhala za ansembe.+ Ufa wanu wamisere wochokera ku mbewu zanu zoyambirira muziupereka kwa wansembe+ kuti madalitso abwere panyumba yanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena