Agalatiya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso, mfundo yakuti palibe munthu amene angaonedwe ngati wolungama+ ndi Mulungu mwa chilamulo ndi yoonekeratu, chifukwa “wolungama adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.”+ Aefeso 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwa kukoma mtima kwakukulu kumeneku, ndithudi mwapulumutsidwa kudzera m’chikhulupiriro,+ osati mwa inu nokha,+ koma monga mphatso ya Mulungu.+
11 Komanso, mfundo yakuti palibe munthu amene angaonedwe ngati wolungama+ ndi Mulungu mwa chilamulo ndi yoonekeratu, chifukwa “wolungama adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.”+
8 Mwa kukoma mtima kwakukulu kumeneku, ndithudi mwapulumutsidwa kudzera m’chikhulupiriro,+ osati mwa inu nokha,+ koma monga mphatso ya Mulungu.+