Mateyu 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ponyani kapolo wopanda pake ameneyu kunja kumdima. Kumeneko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.’+ Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+
30 Ponyani kapolo wopanda pake ameneyu kunja kumdima. Kumeneko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.’+