1 Petulo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Khalani mfulu,+ koma ufulu wanu usakhale ngati chophimbira zoipa,+ koma monga akapolo a Mulungu.+