1 Petulo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muzicherezana popanda kudandaula.+ 3 Yohane 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, ife tili ndi udindo wolandira bwino anthu amenewa ndi kuwachereza,+ kuti akhale antchito anzathu m’choonadi.+
8 Choncho, ife tili ndi udindo wolandira bwino anthu amenewa ndi kuwachereza,+ kuti akhale antchito anzathu m’choonadi.+