Yohane 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndithudi ndikukuuzani, Kambewu ka tirigu kakapanda kugwa m’nthaka ndi kufa, kamakhalabe kamodzi komweko. Koma kakafa,+ kamadzabala zipatso zambiri.
24 Ndithudi ndikukuuzani, Kambewu ka tirigu kakapanda kugwa m’nthaka ndi kufa, kamakhalabe kamodzi komweko. Koma kakafa,+ kamadzabala zipatso zambiri.