2 Petulo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma pali kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ife tikuyembekezera mogwirizana ndi lonjezo lake, ndipo mmenemo mudzakhala chilungamo.+
13 Koma pali kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ife tikuyembekezera mogwirizana ndi lonjezo lake, ndipo mmenemo mudzakhala chilungamo.+