Salimo 69:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+
9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+