Aroma 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komabe, zonena kuti “anayesedwa+ wolungama” sizinalembedwere iye yekha,+ 1 Akorinto 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano zinthu zimenezi zinali kuwagwera monga zitsanzo, ndipo zinalembedwa kuti zitichenjeze+ ifeyo amene mapeto a nthawi* zino atifikira.+
11 Tsopano zinthu zimenezi zinali kuwagwera monga zitsanzo, ndipo zinalembedwa kuti zitichenjeze+ ifeyo amene mapeto a nthawi* zino atifikira.+