Mateyu 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poyankha iye anati: “Ine sananditumize kwa wina aliyense koma kwa nkhosa zotayika za nyumba ya Isiraeli.”+ Yohane 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anabwera kudziko lakwawo, koma anthu akwawo enieniwo sanamulandire.+
24 Poyankha iye anati: “Ine sananditumize kwa wina aliyense koma kwa nkhosa zotayika za nyumba ya Isiraeli.”+