Genesis 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kudzera mwa mbewu yako,+ mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso* ndithu chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+ Salimo 89:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anati: “Ndachita pangano ndi wosankhidwa wanga.+Ndalumbira kwa Davide mtumiki wanga,+
18 Kudzera mwa mbewu yako,+ mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso* ndithu chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+