1 Akorinto 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Polankhula ndi polalikira, mawu anga sanali okopa, oonetsa nzeru, koma oonetsa mzimu ndi mphamvu,+ 2 Akorinto 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndatero chifukwa mukufunafuna umboni wosonyeza kuti Khristu akulankhuladi mwa ine.+ Iye si wofooka kwa inu koma ndi wamphamvu pakati panu.
3 Ndatero chifukwa mukufunafuna umboni wosonyeza kuti Khristu akulankhuladi mwa ine.+ Iye si wofooka kwa inu koma ndi wamphamvu pakati panu.