Machitidwe 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo gulu lonselo linakhala chete, ndipo linayamba kumvetsera Baranaba ndi Paulo pamene anali kufotokoza zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo pakati pa anthu a mitundu ina.+ 2 Akorinto 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithudi inuyo munaona umboni wakuti ndine mtumwi,+ poona mmene ndinapiririra,+ komanso poona zizindikiro, zodabwitsa, ndi ntchito zamphamvu zimene ndinachita.+
12 Pamenepo gulu lonselo linakhala chete, ndipo linayamba kumvetsera Baranaba ndi Paulo pamene anali kufotokoza zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo pakati pa anthu a mitundu ina.+
12 Ndithudi inuyo munaona umboni wakuti ndine mtumwi,+ poona mmene ndinapiririra,+ komanso poona zizindikiro, zodabwitsa, ndi ntchito zamphamvu zimene ndinachita.+