Machitidwe 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Paulo anawalonjera ndi kuyamba kuwafotokozera mwatsatanetsatane+ zimene Mulungu anachita pakati pa anthu a mitundu ina kudzera mu utumiki wake.+ 2 Akorinto 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ifeyo tidzadzitamandira, osati pa zinthu zimene zili kunja kwa malire amene tapatsidwa,+ koma pa zinthu zimene zili mkati mwa malire a gawo limene Mulungu anatipatsa pochita kutiyezera, limene analifikitsa mpaka kwanuko.+
19 Paulo anawalonjera ndi kuyamba kuwafotokozera mwatsatanetsatane+ zimene Mulungu anachita pakati pa anthu a mitundu ina kudzera mu utumiki wake.+
13 Koma ifeyo tidzadzitamandira, osati pa zinthu zimene zili kunja kwa malire amene tapatsidwa,+ koma pa zinthu zimene zili mkati mwa malire a gawo limene Mulungu anatipatsa pochita kutiyezera, limene analifikitsa mpaka kwanuko.+