Deuteronomo 28:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 “Koma mwamuna wolobodoka nkhongono ndi wachisasati* pakati panu, adzayang’ana ndi diso+ loipa m’bale wake, mkazi wake wokondedwa ndi ana ake aamuna amene atsala, 2 Timoteyo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 osakonda achibale awo,+ osafuna kugwirizana ndi anzawo,+ onenera anzawo zoipa,+ osadziletsa, oopsa,+ osakonda zabwino,+
54 “Koma mwamuna wolobodoka nkhongono ndi wachisasati* pakati panu, adzayang’ana ndi diso+ loipa m’bale wake, mkazi wake wokondedwa ndi ana ake aamuna amene atsala,
3 osakonda achibale awo,+ osafuna kugwirizana ndi anzawo,+ onenera anzawo zoipa,+ osadziletsa, oopsa,+ osakonda zabwino,+