Salimo 50:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi zonse ukaona wakuba unali kusangalala naye.+Ndipo unali kugwirizana ndi anthu achigololo.+ Hoseya 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo amasangalatsa mfumu ndi zoipa zawo, ndiponso amasangalatsa akalonga ndi chinyengo chawo.+